Deuteronomo 23:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mukamanga msasa kuti mumenyane ndi adani anu, muzipewa chilichonse chodetsa.*+