Deuteronomo 23:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chifukwa Yehova Mulungu wanu akuyendayenda mumsasa wanu+ kuti akupulumutseni ndi kupereka adani anu mʼmanja mwanu. Choncho msasa wanu uzikhala woyera,+ kuti asaone choipa chilichonse pakati panu nʼkusiya kuyenda nanu limodzi.
14 Chifukwa Yehova Mulungu wanu akuyendayenda mumsasa wanu+ kuti akupulumutseni ndi kupereka adani anu mʼmanja mwanu. Choncho msasa wanu uzikhala woyera,+ kuti asaone choipa chilichonse pakati panu nʼkusiya kuyenda nanu limodzi.