Deuteronomo 23:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iye azikhala pakati panu pamalo alionse amene angasankhe mu umodzi mwa mizinda yanu, kulikonse kumene wakonda. Ndipo musamamuzunze.+
16 Iye azikhala pakati panu pamalo alionse amene angasankhe mu umodzi mwa mizinda yanu, kulikonse kumene wakonda. Ndipo musamamuzunze.+