Deuteronomo 23:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Musamabweretse malipiro a hule lalikazi kapena malipiro a hule lalimuna* mʼnyumba ya Yehova Mulungu wanu kuti mukwaniritse lonjezo lililonse, chifukwa malipiro onsewo ndi onyansa kwa Yehova Mulungu wanu. Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:18 Nsanja ya Olonda,2/1/1997, tsa. 294/15/1989, tsa. 3
18 Musamabweretse malipiro a hule lalikazi kapena malipiro a hule lalimuna* mʼnyumba ya Yehova Mulungu wanu kuti mukwaniritse lonjezo lililonse, chifukwa malipiro onsewo ndi onyansa kwa Yehova Mulungu wanu.