Deuteronomo 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Munthu asamalande mnzake mphero kapena mwala waungʼono woperera ngati chikole cha ngongole,+ chifukwa kutenga zinthu zimenezi kuli ngati kutenga moyo wa munthu ngati chikole. Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:6 Nsanja ya Olonda,6/1/2014, tsa. 79/15/2004, tsa. 26
6 Munthu asamalande mnzake mphero kapena mwala waungʼono woperera ngati chikole cha ngongole,+ chifukwa kutenga zinthu zimenezi kuli ngati kutenga moyo wa munthu ngati chikole.