Deuteronomo 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Musamapotoze chiweruzo cha mlandu wa mlendo kapena mlandu wa mwana wamasiye,+ ndipo musamalande chovala cha mkazi wamasiye kuti chikhale chikole.+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:17 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),2/2019, tsa. 24
17 Musamapotoze chiweruzo cha mlandu wa mlendo kapena mlandu wa mwana wamasiye,+ ndipo musamalande chovala cha mkazi wamasiye kuti chikhale chikole.+