Deuteronomo 24:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Muzikumbukira kuti munali akapolo mʼdziko la Iguputo, ndipo Yehova Mulungu wanu anakuwombolani kumeneko.+ Nʼchifukwa chake ndikukulamulani kuti muzichita zimenezi.
18 Muzikumbukira kuti munali akapolo mʼdziko la Iguputo, ndipo Yehova Mulungu wanu anakuwombolani kumeneko.+ Nʼchifukwa chake ndikukulamulani kuti muzichita zimenezi.