-
Deuteronomo 24:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Mukamakolola mphesa mʼmunda wanu, musamabwerere kukakunkha zotsala. Mphesa zotsalazo zizikhala za mlendo wokhala mʼdziko lanu, mwana wamasiye ndi mkazi wamasiye.
-