Deuteronomo 25:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Amuna akakangana azipita kwa oweruza,+ oweruzawo azigamula mlanduwo. Wolungama azimuweruza kuti alibe mlandu ndipo woipa azimuweruza kuti ali ndi mlandu.+
25 “Amuna akakangana azipita kwa oweruza,+ oweruzawo azigamula mlanduwo. Wolungama azimuweruza kuti alibe mlandu ndipo woipa azimuweruza kuti ali ndi mlandu.+