Deuteronomo 25:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ngati woipayo akuyenera kukwapulidwa,+ woweruza azilamula kuti woipayo amugoneke pansi, ndipo azimukwapula pamaso pa woweruzayo. Azimukwapula zikwapu zogwirizana ndi choipa chimene wachita.
2 Ngati woipayo akuyenera kukwapulidwa,+ woweruza azilamula kuti woipayo amugoneke pansi, ndipo azimukwapula pamaso pa woweruzayo. Azimukwapula zikwapu zogwirizana ndi choipa chimene wachita.