Deuteronomo 25:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mwana woyamba amene mkaziyo angabereke, azitenga dzina la mwamuna womwalira uja,+ kuti dzina la mʼbale wake lisathe mu Isiraeli.+
6 Mwana woyamba amene mkaziyo angabereke, azitenga dzina la mwamuna womwalira uja,+ kuti dzina la mʼbale wake lisathe mu Isiraeli.+