Deuteronomo 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 mkazi wamasiyeyo aziyandikira mchimwene wa mwamuna wakeyo akuluwo akuona ndipo azimuvula nsapato+ nʼkumulavulira kumaso nʼkunena kuti, ‘Izi nʼzimene ziyenera kuchitikira munthu amene wakana kumanga nyumba ya mchimwene wake.’ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:9 Nsanja ya Olonda,9/15/2004, tsa. 26
9 mkazi wamasiyeyo aziyandikira mchimwene wa mwamuna wakeyo akuluwo akuona ndipo azimuvula nsapato+ nʼkumulavulira kumaso nʼkunena kuti, ‘Izi nʼzimene ziyenera kuchitikira munthu amene wakana kumanga nyumba ya mchimwene wake.’