Deuteronomo 25:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mʼthumba lanu musamakhale miyezo iwiri yosiyana yoyezera kulemera kwa chinthu,+ musamakhale ndi muyezo waukulu ndi wina waungʼono.
13 Mʼthumba lanu musamakhale miyezo iwiri yosiyana yoyezera kulemera kwa chinthu,+ musamakhale ndi muyezo waukulu ndi wina waungʼono.