Deuteronomo 25:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Muzikhala ndi muyezo wolondola ndi woyenera woyezera kulemera kwa chinthu komanso muyezo wolondola ndi woyenera woyezera kuchuluka kwa zinthu, kuti masiku anu achuluke mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani.+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:15 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),8/2022, tsa. 27
15 Muzikhala ndi muyezo wolondola ndi woyenera woyezera kulemera kwa chinthu komanso muyezo wolondola ndi woyenera woyezera kuchuluka kwa zinthu, kuti masiku anu achuluke mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani.+