-
Deuteronomo 25:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Iwo anakumana nanu panjira nʼkupha anthu onse amene ankayenda movutika kumbuyo kwanu. Iwo anachita izi pamene munali olefuka ndi otopa ndipo sanaope Mulungu.
-