Deuteronomo 25:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiye Yehova Mulungu wanu akadzakupumitsani kwa adani anu onse okuzungulirani, mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti mulitenge kukhala cholowa chanu,+ mudzafafanize dzina la Aamaleki pansi pa thambo.+ Musadzaiwale zimenezi. Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:19 Tsanzirani, tsa. 144 Nsanja ya Olonda,1/1/2012, tsa. 29
19 Ndiye Yehova Mulungu wanu akadzakupumitsani kwa adani anu onse okuzungulirani, mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani kuti mulitenge kukhala cholowa chanu,+ mudzafafanize dzina la Aamaleki pansi pa thambo.+ Musadzaiwale zimenezi.