Deuteronomo 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako mukakawoloka, mukalembe pamiyalapo mawu onse a mʼChilamulo ichi, kuti mulowe mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani, dziko loyenda mkaka ndi uchi, mogwirizana ndi zimene Yehova, Mulungu wa makolo anu anakulonjezani.+
3 Kenako mukakawoloka, mukalembe pamiyalapo mawu onse a mʼChilamulo ichi, kuti mulowe mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani, dziko loyenda mkaka ndi uchi, mogwirizana ndi zimene Yehova, Mulungu wa makolo anu anakulonjezani.+