Deuteronomo 27:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Mose komanso ansembe omwe ndi Alevi analankhula ndi Aisiraeli onse kuti: “Aisiraeli inu, khalani chete ndi kumvetsera. Lero mwakhala anthu a Yehova Mulungu wanu.+
9 Kenako Mose komanso ansembe omwe ndi Alevi analankhula ndi Aisiraeli onse kuti: “Aisiraeli inu, khalani chete ndi kumvetsera. Lero mwakhala anthu a Yehova Mulungu wanu.+