Deuteronomo 27:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Mukawoloka Yorodano, mafuko otsatirawa ndi amene adzaimirire paphiri la Gerizimu+ nʼkudalitsa anthu: Fuko la Simiyoni, Levi, Yuda, Isakara, Yosefe ndi Benjamini. Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:12 Nsanja ya Olonda,2/1/1997, ptsa. 30-316/15/1996, tsa. 14
12 “Mukawoloka Yorodano, mafuko otsatirawa ndi amene adzaimirire paphiri la Gerizimu+ nʼkudalitsa anthu: Fuko la Simiyoni, Levi, Yuda, Isakara, Yosefe ndi Benjamini.