Deuteronomo 27:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndipo mafuko otsatirawa ndi amene adzaimirire paphiri la Ebala+ kuti azidzavomereza matemberero akamadzatchulidwa: Fuko la Rubeni, Gadi, Aseri, Zebuloni, Dani ndi Nafitali. Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:13 Nsanja ya Olonda,2/1/1997, ptsa. 30-316/15/1996, tsa. 14
13 Ndipo mafuko otsatirawa ndi amene adzaimirire paphiri la Ebala+ kuti azidzavomereza matemberero akamadzatchulidwa: Fuko la Rubeni, Gadi, Aseri, Zebuloni, Dani ndi Nafitali.