Deuteronomo 28:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ana anu+ adzakhala odalitsika* komanso chipatso cha mʼdziko lanu, ana a ziweto zanu, ana a ngʼombe zanu ndi ana a nkhosa zanu adzakhala odalitsika.+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:4 Nsanja ya Olonda,6/15/1996, ptsa. 15-16
4 Ana anu+ adzakhala odalitsika* komanso chipatso cha mʼdziko lanu, ana a ziweto zanu, ana a ngʼombe zanu ndi ana a nkhosa zanu adzakhala odalitsika.+