Deuteronomo 28:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova adzadalitsa nyumba zanu zosungiramo zinthu+ komanso chilichonse chimene mukuchita ndipo adzakudalitsani mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani.
8 Yehova adzadalitsa nyumba zanu zosungiramo zinthu+ komanso chilichonse chimene mukuchita ndipo adzakudalitsani mʼdziko limene Yehova Mulungu wanu akukupatsani.