Deuteronomo 28:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova adzakupangani kukhala anthu ake oyera,+ mogwirizana ndi zimene analumbira kwa inu,+ chifukwa mukupitiriza kusunga malamulo a Yehova Mulungu wanu ndipo mukuyenda mʼnjira zake.
9 Yehova adzakupangani kukhala anthu ake oyera,+ mogwirizana ndi zimene analumbira kwa inu,+ chifukwa mukupitiriza kusunga malamulo a Yehova Mulungu wanu ndipo mukuyenda mʼnjira zake.