Deuteronomo 28:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova adzakupatsani ana ambiri komanso ziweto zochuluka ndipo nthaka+ yamʼdziko limene Yehova analumbira kwa makolo anu kuti adzakupatsani, idzabereka zipatso zambiri.+
11 Yehova adzakupatsani ana ambiri komanso ziweto zochuluka ndipo nthaka+ yamʼdziko limene Yehova analumbira kwa makolo anu kuti adzakupatsani, idzabereka zipatso zambiri.+