Deuteronomo 28:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova adzakuchititsani kuti mukhale mutu osati mchira ndipo mudzakhala pamwamba+ osati mʼmunsi, mukapitiriza kumvera malamulo a Yehova Mulungu wanu amene ndikukupatsani lero kuti muziwasunga ndi kuwatsatira.
13 Yehova adzakuchititsani kuti mukhale mutu osati mchira ndipo mudzakhala pamwamba+ osati mʼmunsi, mukapitiriza kumvera malamulo a Yehova Mulungu wanu amene ndikukupatsani lero kuti muziwasunga ndi kuwatsatira.