Deuteronomo 28:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yehova adzakulangani ndi chifuwa chachikulu, kutentha kwa thupi koopsa,+ kutupa, nyengo yotentha,* lupanga,+ mphepo yotentha yowononga mbewu ndi matenda a mbewu.+ Zimenezi zidzakuvutitsani mpaka mutatheratu.
22 Yehova adzakulangani ndi chifuwa chachikulu, kutentha kwa thupi koopsa,+ kutupa, nyengo yotentha,* lupanga,+ mphepo yotentha yowononga mbewu ndi matenda a mbewu.+ Zimenezi zidzakuvutitsani mpaka mutatheratu.