Deuteronomo 28:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mitembo yanu idzakhala chakudya cha mbalame zonse zouluka mumlengalenga ndi zilombo zoyenda panthaka, ndipo sipadzapezeka woziopseza.+
26 Mitembo yanu idzakhala chakudya cha mbalame zonse zouluka mumlengalenga ndi zilombo zoyenda panthaka, ndipo sipadzapezeka woziopseza.+