Deuteronomo 28:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yehova adzakulangani ndi zithupsa za ku Iguputo, matenda a mudzi,* ziwengo ndi zotupa, ndipo simudzachira matenda amenewa.
27 Yehova adzakulangani ndi zithupsa za ku Iguputo, matenda a mudzi,* ziwengo ndi zotupa, ndipo simudzachira matenda amenewa.