Deuteronomo 28:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Yehova adzakulangani ndi misala, khungu+ ndipo adzakuchititsani kuti musokonezeke.