Deuteronomo 28:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ana anu aamuna ndi ana anu aakazi adzaperekedwa kwa anthu ena+ inu mukuona ndipo nthawi zonse mudzalakalaka mutawaona, koma manja anu adzakhala opanda mphamvu.
32 Ana anu aamuna ndi ana anu aakazi adzaperekedwa kwa anthu ena+ inu mukuona ndipo nthawi zonse mudzalakalaka mutawaona, koma manja anu adzakhala opanda mphamvu.