-
Deuteronomo 28:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Yehova adzakulangani ndi zithupsa zopweteka komanso zosachiritsika mʼmawondo ndi miyendo yanu. Matendawa adzayambira kumapazi mpaka paliwombo.
-