Deuteronomo 28:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Mudzadzala mbewu zambiri mʼmunda, koma mudzakolola zochepa+ chifukwa dzombe lidzadya mbewuzo.