Deuteronomo 28:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Mudzabereka ana aamuna ndi aakazi, koma sadzakhala anu chifukwa adzatengedwa kupita ku ukapolo.+