Deuteronomo 28:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Matemberero onsewa+ adzakugwerani ndipo zinthu zoipa zonsezi zidzakuchitikirani mpaka mutawonongedwa,+ chifukwa simunamvere mawu a Yehova Mulungu wanu posunga malamulo ndi malangizo amene anakupatsani.+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:45 Nsanja ya Olonda,1/15/1995, ptsa. 15-16
45 Matemberero onsewa+ adzakugwerani ndipo zinthu zoipa zonsezi zidzakuchitikirani mpaka mutawonongedwa,+ chifukwa simunamvere mawu a Yehova Mulungu wanu posunga malamulo ndi malangizo amene anakupatsani.+