Deuteronomo 28:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Yehova adzakutumizirani adani anu kuti akuukireni ndipo mudzawatumikira+ muli ndi njala,+ ludzu, usiwa ndiponso mukusowa chilichonse. Iye adzakuvekani goli lachitsulo mʼkhosi lanu mpaka atakuwonongani.
48 Yehova adzakutumizirani adani anu kuti akuukireni ndipo mudzawatumikira+ muli ndi njala,+ ludzu, usiwa ndiponso mukusowa chilichonse. Iye adzakuvekani goli lachitsulo mʼkhosi lanu mpaka atakuwonongani.