Deuteronomo 28:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Adzakuzungulirani nʼkukutsekerani mʼmizinda yanu* mʼdziko lanu lonse, mpaka mipanda yanu yaitali ndi yolimba kwambiri imene mukuidalira itagwa. Adzakuzungulirani ndithu mʼmizinda yanu yonse mʼdziko lanu limene Yehova Mulungu wanu wakupatsani.+
52 Adzakuzungulirani nʼkukutsekerani mʼmizinda yanu* mʼdziko lanu lonse, mpaka mipanda yanu yaitali ndi yolimba kwambiri imene mukuidalira itagwa. Adzakuzungulirani ndithu mʼmizinda yanu yonse mʼdziko lanu limene Yehova Mulungu wanu wakupatsani.+