56 Ndipo mkazi amene anakulira moyo wofewa komanso wachisasati pakati panu, amene sanayambe waganizapo zopondetsa phazi lake pansi chifukwa chokulira moyo wofewa, sadzamvera chisoni mwamuna wake wokondedwa,+ mwana wake wamwamuna komanso mwana wake wamkazi.