-
Deuteronomo 28:57Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
57 Iye sadzafuna kugawana nawo zotuluka mʼmimba mwake pambuyo pobereka komanso mnofu wa ana ake aamuna amene wabereka, popeza adzawadya mobisa chifukwa cha mavuto oopsa amene mudzakumane nawo adani anu akadzazungulira mizinda yanu.
-