Deuteronomo 28:59 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Yehova adzabweretsa miliri yoopsa pa inu ndi ana anu. Miliri imeneyo idzakhala yaikulu kwambiri ndi yokhalitsa,+ ndipo mudzagwidwa ndi matenda oopsa komanso okhalitsa.
59 Yehova adzabweretsa miliri yoopsa pa inu ndi ana anu. Miliri imeneyo idzakhala yaikulu kwambiri ndi yokhalitsa,+ ndipo mudzagwidwa ndi matenda oopsa komanso okhalitsa.