-
Deuteronomo 28:61Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
61 Kuwonjezera pamenepo, Yehova adzakubweretserani matenda aliwonse ndi mliri uliwonse umene sunalembedwe mʼbuku la Chilamulo ili, mpaka mutawonongedwa.
-