Deuteronomo 28:62 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Ngakhale kuti mwachuluka ngati nyenyezi zakumwamba,+ mudzatsala ochepa+ chifukwa chakuti simunamvere mawu a Yehova Mulungu wanu.
62 Ngakhale kuti mwachuluka ngati nyenyezi zakumwamba,+ mudzatsala ochepa+ chifukwa chakuti simunamvere mawu a Yehova Mulungu wanu.