-
Deuteronomo 28:66Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
66 Moyo wanu udzakhala pangozi yaikulu koopsa, ndipo mudzakhala mwamantha usiku ndi masana, moti simudzakhala wotsimikiza ngati mudzakhalebe ndi moyo.
-