-
Deuteronomo 28:67Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
67 Mʼmawa mudzanena kuti, ‘Zikanakhala bwino akanakhala madzulo!’ ndipo madzulo mudzanena kuti, ‘Zikanakhala bwino ukanakhala mʼmawa!’ chifukwa cha mantha amene adzagwire mtima wanu, ndiponso chifukwa cha zimene maso anu adzaone.
-