-
Deuteronomo 28:68Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
68 Yehova adzakubwezerani ku Iguputo pasitima kudzera njira imene ndinakuuzani kuti, ‘Simudzaionanso.’ Kumeneko mudzalakalaka kudzigulitsa kwa adani anu kuti mukhale akapolo aamuna ndi aakazi, koma sipadzakhala wokugulani.”
-