Deuteronomo 29:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho Mose anaitana Aisiraeli onse nʼkuwauza kuti: “Inu munaona ndi maso anu mʼdziko la Iguputo zonse zimene Yehova anachitira Farao, atumiki ake onse ndi dziko lake lonse,+
2 Choncho Mose anaitana Aisiraeli onse nʼkuwauza kuti: “Inu munaona ndi maso anu mʼdziko la Iguputo zonse zimene Yehova anachitira Farao, atumiki ake onse ndi dziko lake lonse,+