-
Deuteronomo 29:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Simunadye mkate, simunamwe vinyo kapena zakumwa zina zoledzeretsa, kuti mudziwe kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu.’
-