Deuteronomo 29:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiyeno munafika pamalo ano, ndipo Sihoni mfumu ya Hesiboni+ ndi Ogi mfumu ya Basana+ anabwera kudzamenyana nafe, koma tinawagonjetsa.+
7 Ndiyeno munafika pamalo ano, ndipo Sihoni mfumu ya Hesiboni+ ndi Ogi mfumu ya Basana+ anabwera kudzamenyana nafe, koma tinawagonjetsa.+