-
Deuteronomo 29:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Nonsenu mwaima pano lero pamaso pa Yehova Mulungu wanu, inu atsogoleri a mafuko, akulu anu, atsogoleri anu, mwamuna aliyense wa mu Isiraeli,
-