Deuteronomo 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 ana anu, akazi anu,+ mlendo+ amene akukhala mumsasa wanu, kuyambira amene amakutolerani nkhuni mpaka amene amakutungirani madzi.
11 ana anu, akazi anu,+ mlendo+ amene akukhala mumsasa wanu, kuyambira amene amakutolerani nkhuni mpaka amene amakutungirani madzi.