Deuteronomo 29:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu muli pano kuti mulumbire nʼkuchita pangano ndi Yehova Mulungu wanu, pangano limene Yehova Mulungu wanu akuchita nanu lero.+
12 Inu muli pano kuti mulumbire nʼkuchita pangano ndi Yehova Mulungu wanu, pangano limene Yehova Mulungu wanu akuchita nanu lero.+